Barry Uno

Pola Moto (feat. Nepman) [Radio Edit]

barry uno pola moto (feat. nepman) [radio edit] şarkı sözleri

Na na na nayiiiiiii Uno Yeah Huh Zili pa mphuno Viyaaaaa Eyaaa ihh yeahh ih yeahhh Nepi Maa ya ya yaaayiiii Chonde pola moto Mobodza toto Phokoso toto Pola moto to to Nkhondo ine toto Mavuvu toto Pola moto to to Aahhh pachiyambi tinali bho Magaye amatisimba chi couple cha nyo Mbiri yathu inali bho unali mkazi wa bho Wa ulemu wodekha chi mami cha nyo Koma lero umangondiyalusa Pa line ndi ya ife moti tinatchuka Umangobwebwetuka anthu kutiweluza Mamveramvera ako ndi awa akutizunza Azinzako njoka madolo Daily kusintha amuna banja samalifuna Kwawo ndikupasula lero ndi izo akuzembera wako iwe tachangamuka Chonde nkhondo no pola moto eyaa Nkhondo nkhondo no pola moto ummm Pola moto pola mo... Po pola moto pola mo Po pola moto pola mo Po pola moto Pola motoooooo Daily drama daily nkhondo Kukangana daily moto Kunyoza abale anga daily pokopoko Kukhala nawe ndi chitonzo Ndithu anthu amasintha Moti chikondi chonse chimapita Ma plan amasintha lokakamiza limaswa mphika Zandilaka ndachimina Daily ma fever bp nkhani mpungwe mpungwe Nsanje zozilengera nkhani zondipekela Kaya ndiku-topa nane bola kungonena Moyo wa nzako si macheza Mtima umasweka kupilira kokha nde ndayesesa Mwina ndi social media yi ikupusisa Chonde pola moto nkhondo to to Ayi ndithu ndayesesa Chonde nkhondo no pola moto eyaa Nkhondo nkhondo no pola moto ummm Pola moto pola mo... Po pola moto pola mo Po pola moto pola mo Po pola moto Pola motoooooo Ine toto Zachigulu pa nyumba anthu thot ho Ndakana toto Uzalira mayi ine Kalanga koto eyaiiii mmhhhh Shode nkhondo no pola moto eyaaa Nkhondo nkhondo no pola motoo mmmhhh Pola moto pola mo... Po pola moto pola mo Po pola moto pola mo Po pola moto Pola motoooooo Pola moto pola mo... Po pola moto pola mo Po pola moto pola mo Po pola moto Pola motoooooo
Sanatçı: Barry Uno
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 2:57
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Barry Uno hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı