baxxy mw munthu ndi mphwake şarkı sözleri

Iweee, iweee Wina afapo Apapa tikanganapo Wina afapo Tipezeka tagwiranapo Aliyense azipanga zake Siife munthu ndi m'phwake Aliyense azipanga zake Siife munthu ndi m'phwake Aliyense azipanga zake Mukundilowatu mchala Kundikandatu pa bala Kuputa moto munthu ndangoKhala Kenaka uzitititi tikukunyala Ukumachezatu mopusa aise Ukumayankhula mokhuta aise Malingana ndi zomwe tikudutsa ife Anthu tikumayenda olusa aise Nde osamandijayila, osamandijayila Madhala ali ndi maizemill mabwande ndikugayila Uzindikira ukudzuka uli ku Bwaila Mfanayu si lamya koma mmene amutchayila You know how I be (Bee), kundiputa ndi mbola Different kind of animal, osamandicaller (khola) Unless ndiwe photographer,osamanditola Unless ndiwe photographer, osamandi... Wina afapo Apapa tikanganapo Wina afapo Tipezeka tagwiranapo Aliyense azipanga zake Siife munthu ndi m'phwake Aliyense azipanga zake Siife munthu ndi m'phwake Aliyense azipanga zake
Sanatçı: Baxxy Mw
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 2:09
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Baxxy Mw hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı