c.h.r.i.m tate (feat. samziya & tracy) şarkı sözleri

Tate ndinu Mulungu osalephera Mmoyomu tili nawo abwenzi Otikonda tikakhala ndi khobidi Zikavuta amasintha njira Koma inu yesu simsintha Chikondi chanu chopanda malire Mmatikonda nthawi zonse Koma inu mbuye chikondi chanu sichisintha Mumatikonda tonse Mosawerengera mphulupulu zathuuu Tate ndinu Mulungu osalephera Tate ndinu chikondi chopanda malire Mwandivuula mmatope Kundichotsa kum'dima Mwandisambitsa thupi lonse Kundidzodza M'kuwala Tate ndinu Mulungu osalephera Tate ndinu chikondi chopanda malire I still remember the days of wind chase and blind devotion Racing in the motions of life without direction Ndikomwe munandichotsa Bhawa ndi ma babe felt like they made sense koma sizimakwanira Ndinali kamfana koma ndinkazimva kujayira Ena akati uwu moto ndimafuna nditagwira Chiphe samalawa koma ndimafuna nditafira Munandilekelera munthawi yakusadziwa Mwateteza muzambiri bwenzi pano nditadhiwa Matsiku a one for sorry oona imodzi njiwa But Now I know for sure that Yesu ndiye njira Katakwe nsanamangwe enawa amangojoker Sindikudziwa ndingathe bwanji chikondichi chitachoka Ndimaopa cause ndinu mphamvu yanga ndikafoka Munkhondo yanga ndi satana mivi mumabloka Zimangovuta but you deserve my best For all the curses you hexed So we can get a shot at that amazing eternal rest The only King who faced sin and prevailed the test Ambuye your love is great Kwathu ndikuthokoza cause you never change Where would I be without you Lord? Somebody tell me. Somebody Where would I be without you Lord? Somebody tell me Somebody I'll be lost in the gutter where no one would ever find me Trapped in my sin barricaded and drowning Where would I be without you Lord? Somebody tell me somebody Where would I be without you Lord? Somebody tell me Somebody Tate ndinu Mulungu osalephera Tate ndinu chikondi chopanda malire Mwandivuula mmatope Kundichotsa kun'dima Mwandisambitsa thupi lonse Kundidzodza M'kuwala Tate ndinu Mulungu osalephera Tate ndinu chikondi chopanda malire
Sanatçı: C.H.R.I.M
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:19
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
C.H.R.I.M hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı