daliewayve moyo ndi wokoma şarkı sözleri
Tangodutsa
Ayamba kale zinkhani
Sanatiyankhuleko
Koma kuti ndife amatama
Ndi chani?
I know that you hate me
Bro tell me wagwan
Cause I do not hate no man
(Yes I do not hate no)
Lemme live my life
Moyo ndi wokoma
I have been through a lot
Ndakumana ndizokhoma
Lemme live my life
Moyo ndi wokoma
I have been through a lot
Ndakumana ndizokhoma
Trust nobody
Focus on nobody
Just be yourself
You don't need nobody else
Panga zako
Amakuyenda pansi ndi anzako
Panga zako
Amakuyenda pansi ndi anzako
Tangodutsa
Ayamba kale zinkhani
Sanatiyankhuleko
Koma kuti ndife amatama
Ndi chani?
I know that you hate me
Bro tell me wagwan
Cause I do not hate no man
(Yes I do not hate no)
Lemme live my life
Moyo ndi wokoma
I have been through a lot
Ndakumana ndizokhoma
Lemme live my life
Moyo ndi wokoma
I have been through a lot
Ndakumana ndizokhoma
Just get your paper
Dont care bout' a hater
Get your cheddah
Asiye azijeda
Azijeda
Asiye azijeda
Tangodutsa
Ayamba kale zinkhani
Sanatiyankhuleko
Koma kuti ndife amatama
Ndi chani?
I know that you hate me
Bro tell me wagwan
Cause I do not hate no man
(Yes I do not hate no)
Lemme live my life
Moyo ndi wokoma
I have been through a lot
Ndakumana ndizokhoma
Lemme live my life
Moyo ndi wokoma
I have been through a lot
Ndakumana ndizokhoma

