ebel delilah (feat. mr shine) şarkı sözleri
Oowoooo Ebel
Nanananana Mr Shine
Iwe beibe ndiwe okongola kufanana iwe ndi Delilah nkhope yokongola iwe
Ukamamwetulira iwe beibe tima dimples nso nkuchimake ayi ndakukonda iwe
Iwe beibe ndiwe okongola kufanana iwe ndi Delilah nkhope yokongola iwe
Eeeh yeaaah aaaah
Beibe uuuummmh
Aaahaa
Ndiwe okongola
Nzanga ndiwe nthiti yanga ndiwee aaaaah
Usanamizidweee
I will never leave you aaaah
Usaganize zanu filimu izi
Zamu filimu
Koma izi nzenizeni
Usazitenge zama sewera izi zamasewera
Ayi chikondi chenicheni
Beibe iwe ndi ine ndithu tikudyerera
Tili awiriwiriwiri tiku mwerera
Iwe ndiine beibe bri bri bri
Then makes our life easier
Beibe ndikudziwa kuti umandikonda and I promise kuti sudzawonda
And I promise kuti sudzawonda
Iwe ndi ine beibe bri bri bri
Vuma vuma Ntombi yemhlophe
Vuma
Vuma ubengowami
Vuma sibe moya omunye vuma
nkanyezi yokusa
Vuma vuma Ntombi yemhlophe
Vuma
Vuma ubengowami
Vuma sibe moya omunye vuma
nkanyezi yokusa
Nzanga ndiwe nthiti yanga ndiwee aaaaah
Usanamizidweee
I will never leave you aaaah
Usaganize zanu filimu izi
Zamu filimu
Koma izi nzenizeni
Usazitenge zama sewera izi zamasewera
Ayi chikondi chenicheni
Nzanga ndiwe ooowyahh
Nthiti yanga ndiwee beibe
Wanga ndiwe beibe
Usanamizidwe eeeyeah I will never leave you ooowyeah aaaah
Usaganize zamu filimu izi zamu filimu
Koma izi ndizenizeni
Usazitenge zama sewera izi zamasewera ayi chikondi chenicheni