ebel ndimakukonda şarkı sözleri
Ohooo wooo
Owooo Hooo
Ebel Gaxybo you know
Ndimakukonda honey iwe okay
Owuwooo ndimakukonda yah babe it's me again eheee ndimakukonda okay
Ndati ndikuwuze ndima kukonda ndimtima wanga wonse
Ndimakukonda
Nditsimikizire umandakonda
Kuyambira kale ndinkakukonda
Palibe kusintha ndidzakukonda
Mpakana kale kale ndidzakukonda
Tatiye kwathu iweeee
Ndimakukonda babe
Ngithanda wena wedwa
Ndimakukonda honey owuwuwoo
Ngithanda wena wedwa
Ndimtima wanga wonse
Nhliziyo Yami yonke
Ndimakukonda honey
Oowwww
Ngithanda wena wedwa
Ukamati umandakonda ine kumtimaku myaaaa
Iwe ndi ine together mpaka mwana alire Ng'aaaa tsiku loyamba ntangokuwona mpaka diso langa ng'ala
Nkuwona sindina chedwe nangopanga zongo mara
Koma usapusisike nzama social media
Ngadzadzese mpungwempungwe banja lathu Liliya
Ungadzawone Zina m'menemo nkuyamba kusilira
Basi mtima kukopeka ineyo nkundisiya
Asakupusitse mayoo ndi mbatcha zobwereka
Anabwera ndiyongonama kuti anali ku Amereka
Koma amadzangokuthawa ukagwetsa bereka
Kusiya ukutuwa ukusowa mchereka yooo
I don't wanna loose whole my life I will spend with you am ready to die for you I swear I will never cheat on you
It's me again
Ndimakukonda babe
Ngithanda wena wedwa
Ndimakukonda honey owuwuwoo
Ngithanda wena wedwa
Ndimtima wanga wonse
Nhliziyo Yami yonke
Ndimakukonda honey
Oowwww
Ngithanda wena wedwa
Ngakhale zokoma zinga churukee
Chikondi changa babe nchopanda malire
Monga kaduwa kumawa kachiwalire
Tandilora babe ayi ndiku file
Tatiye kwanu honey akandione
Popeza kwathu honey amakukonda
Tatiye kwathu iwe
Ndimakukonda babe
Ngithanda wena wedwa
Ndimakukonda honey owuwuwoo
Ngithanda wena wedwa
Ndimtima wanga wonse
Nhliziyo Yami yonke
Ndimakukonda honey
Oowwww
Ngithanda wena wedwa
Ndimakukonda babe
Ngithanda wena wedwa
Ndimakukonda honey owuwuwoo
Ngithanda wena wedwa
Ndimtima wanga wonse
Nhliziyo Yami yonke
Ndimakukonda honey
Oowwww
Ngithanda wena wedwa