edgar kapiza bayani pamaso pa inu maria şarkı sözleri
Pa maso pa inu Maria (Before you Mother Mary)
Timakonda kusonkhana (We love to come)
Kuti tichite mapemphero (To pray)
Ndikukauza mafuno (And tell you our needs)
Ndinu a mayi a Mulungu (You are mother of God)
Ndi amayi athu (And our mother too)
Zinthu zonse tizisowa (All those things we need)
Osamana (Obtain for us)
Mudalitsetu olemera (Bless the rich)
Muthandize osauka (Help the poor)
Mulimbitse opanda mphavu (Strengthen the weak)
Musungitse moyo wathu (Safely keep our lives)
Tikhale anthu ofatsa (That we be meek and gentle)
Oyera mtima (With pure hearts)
Zoyipa zonse zakale (All our old sinful ways)
Tizisiye (We must abandon)
Mumasekera m'paradizo (You are in heaven)
Muli Mfumu ya anjelo (You are the Queen of angels)
Tikufuna kukhala nanu (We yearn to join you)
Ndikulowa mdziko lanu (And enter into your heavenly kingdom)
Tsiku limene lakufa (On our time of death)
Nthawi ya mkhawa (That dreaded time)
Muperekeze kwa Yesu ( To Jesus escort us)
Ana anu (We your children)
Kuti anthu a dziko lino (For all peoples)
Akalowe mparadizo (to enter paradise)
Zoipa alekana nazo (They must forsake sin)
Alandire ubatizo (And be baptised)
Mutichitire chisoni (Have mercy on us)
Inu wansinsi (You who welcome every one)
Mutipemphere ife (Pray for us)
Nthawi zonse (Always)
Mutichitire chisoni (Have mercy on us)
Inu wansinsi (You who welcome every one)
Mutipemphere ife (Pray for us)
Nthawi zonse (Always)

