eli njuchi hane şarkı sözleri

Hane kubanja choka samachoka choncho Hane pochoka ngati mukuthawa nkhondo (Hane wapambana) Ndikulira koto (Hane wapambana) Ndikulira koto Hane kubanja choka samachoka choncho Hane pochoka anasiya mpoto pa moto (Hane wapambana) Ndikulira koto (Hane wapambana) Issh koma Hane Hane Hane wapambana Ndikulira Hane Hane wapambana Issh koma Hane Hane Hane wapambana Ndikulira Hane Hane wapambana Issh koma Hane (Tay grin) Oky Rrrad Ati bwanji apa Issh koma Hane Utangochoka Nkhawa, Moti zoona unasiya anawa Uli patsoka Mawa Chozemba chimakumana nchokwawa Unagulitsa ng'ombe zanga zonse Napinyulitsa njinga zanga zonse Kunabwelanso a bank nkhonde Akuti unantapila chingongole Eeh Uli patsoka Hane Ndiwe njoka Hane Mimba m'tsekule ku joni ko Hane Ndalama zanga unapangila chiphaso Issh koma Hane Hane Hane wapambana Ndikulira Hane Hane wapambana Issh koma Hane Hane Hane wapambana Ndikulira Hane Hane wapambana Issh koma Hane
Sanatçı: Eli Njuchi
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 2:59
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Eli Njuchi hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı