general major khalen dear mama (feat. space) şarkı sözleri
Jeah
Break up is nothing just imagine
pushing life without Mother
without father
Dear mama ulendo wanga ndi oyenda ine
Ndi oyenda ndi ntima koma ngakhale pena
Zikavuta ndiyenda mu m'dima koma ndikudziwa kuti ndikafika chifukwa sindiyima
M'manja mwanga muli kalata yodzadza ndi mafuso Dear maa ndayambapo
Kod ndi ulendo wanji osabwelela chonsecho ndiulendo wawufupi
Fanzi imayenda maulendo atali atali kumakafika overseas
Koma inu lelo ama sizii ulendo wanu wama yard ten
Koma pano mukutha zaka ten
Ama ndamaliza ma pen ten kulembela makalata kwa inu koma osayankhidwa mama
One thing you should know
No matter how old i can be olo ine nditamela invii
Sindingakuyiwaleni ama olo ndili ndi ndrama
Daily kudya nyama
Amama amama ah ndilila
Amama amama ah ndilila
Ine ndilila
Amama amama ah ndilila Amama
Dear mama
Amama amama ah ndilila
Amama amama ah ndilila
Ine ndilila
Amama amama ah ndilila Amama
Jeah
Dear mama munandisiya wachichepele
Movutika momwemo ndakula ndi achina tupele
Komabe naye Mulungu mphavu zake sizinachepele
Lelo ndine abambo bambo kulitu ya china Raheem
Ama zidzukulu ndi plenty koma daily zimandifusa mafuso twenty
Kod agogo alikut ine mu ntima kuti dii!!
It's only one thing that brings me back
Always the memories kills me
Koma ndikudziwa ama muliku heaven
Tidzabwela konko ifeyo ku heaven
Tidzakhala limodzi monga banja mu Eden
Ndizidzukulu zanu inuyo Eleven
Tsono nono ine life ya m'ma thalaven
Ndicholinga Mulungu andi save ine
Pamodzi ndi ana anga Seven
Moyo wanga ndaupeleka ah nsembe ine
Moyo wanga ndaupeleka ah nsembe ine
(Moyo wanga ndaupeleka ah nsembe ine)
Amama amama ah ndilila
Amama amama ine ndilila
Amama amama ah ndilila
Amama
(Dear mama)
Amama amama ah ndilila
Amama amama ine ndilila
Amama amama ah ndilila
Amama
Amama amama ah ndilila
Amama amama ine ndilila
Amama amama ah ndilila
Amama
Amama amama ah ndilila
Amama amama ine ndilila
Amama amama ah ndilila
Amama