genii blakk mkazi wapabala şarkı sözleri

Ndaona ubwino wa mkazi wapabala Ngakhale amunene kuti ndi mambala Ubwino wache ndauziwa eh Ona ubwino wa mkazi wapabala Ngakhale amunene kuti ndi mambala Ubwino wake ndauziwa eh Ndimamvana ndi mkazi wapabala Samanyada ndi nkhani ya komwe iye amakhala Samatengera looks kapena zomwe umavala Simunthu wamba chabe naye anamva kuwawa Amachezeka bwino ukamtenga bho Zakwanu m'tembo kwathu m'tembo Amati zausilu no Wakumana ndi ziphinjo so chibwana ndipa zero Kukuchenjeza ikalakwa ngati mu njira simuli bwino Ndipo, ulusi wake amaponya wa khenge Kutelela pamalo ngati pagwera denje Nabola azisake kuti mawa amede Zikoli ndi latonse bolani kangachepe eh Ndaona ubwino wa mkazi wapabala Ngakhale amunene kuti ndi mambala Ubwino wache ndauziwa eh Ona ubwino wa mkazi wapabala Ngakhale amunene kuti ndi mambala Ubwino wake ndauziwa eh Ndimamvana ndi mkazi wapabala Amandilesa kupeza mkazi wachisawawa Uzakhumudwa nthenda ili ndi am'mipandawa Magwiragwira mphwanga uzamva nawo kuwawa eh Timamvana pa nkhaniso ya bawa Samafuna ziwawa bola azisangalala Amandithoka zoba ndi yemwe timamukawa Life is too short time yatha zivaya eh Sikuti naye safuna chikondi Chinamuluma chakuda koma ndi wachikondi Kudyesa ana ake Mpakana abale ake Olo ena amunene iye amapanga zake eh Ndaona ubwino wa mkazi wapabala Ngakhale amunene kuti ndi mambala Ubwino wache ndauziwa eh Ona ubwino wa mkazi wapabala Ngakhale amunene kuti ndi mambala Ubwino wake ndauziwa eh Amati zonse ndizotheka aise Amati zonse ndizotheka aise nabola golide Amati zonse ndizotheka aise Amati zonse ndizotheka aise nabola golide Sinkhani yomakambira kumbali Kusochera kulipo m'manja mwako muli nyali Kumayesa kudekha poyang'ana anamwali Azapezeka easy aise zonse ndi nthawi Amavutika chonchi kamba ka umphawi Ufulu ndi mtendele umasowa mwa amayi Apanga bwanji nanga game ili m'manja mwake Bola lalero liduse iye atapanga zake eh Ndaona ubwino wa mkazi wapabala Ngakhale amunene kuti ndi mambala Ubwino wache ndauziwa eh Ona ubwino wa mkazi wapabala Ngakhale amunene kuti ndi mambala Ubwino wake ndauziwa eh Ubwino wa mkazi wapabala Ngakhale amunene kuti ndi mambala Ubwino wache ndauziwa eh Ona ubwino wa mkazi wapabala Ngakhale amunene kuti ndi mambala Ubwino wake ndauziwa eh Yeah, DMG we keep it real all day DMG we keep it real all day
Sanatçı: Genii Blakk
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:42
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Genii Blakk hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı