henry czar experience şarkı sözleri

Ukaliiiiiii Heeeeee Royal hustle the factory Ndakulandilani chief muma interview muno ine ndi mr czar Ndikufuna mundiyakhe fuso linalililose sindufuna zobisa Ngati mukudziwa kuti muli ndimatukutuku muno sitigwilizana Office ndi yanga introduce yourself mwina mkumvana Ndine henry ndimagela ku chanco Ndinakhoza bwino kuposa anzanga Ngati mukufuna watchito wabho Ine ndilipo zithu ndipanga I dont give a damn about what you are saying Ndayiwona cv sukupangasotu qualify Of course uli degree koma ulibe experience taziwone sunavale tie Experience experience experience (My foot) Experience experience experience (Uko) Experience experience experience (Yachani) Experience experience experience (Ndilibe) Experience (Igwa kumwamba) Experience (Ndingoyitola) Experience (Ibwera yokha) Experience (Ichoka Ku) Experience (Igwa kumwamba) Experience (Ndingoyitola) Experience (Ibwera yokha) Experience (Ichoka Ku) Experience ndipeza bwanji Munthu ine school ndamaliza last year Ntchito ndayisaka town mu Kumangozungulilamo ngati ndine wa masiye Nanga mpaka five years experience Ichoka kuti ndine mwanapiye Mwana wang'ono osakhwima pamchombo Chonde bwana musandisiye Ndimene zikukhalila mma office mu Ngati ulibe experience sukupeza tchitozi Graduates every year mu ma college mu Koma tchito zikusowa lower case in capitals Ena kulowela connection, mpaka connection Eya mumadziwa ndani nkozi Mkazi avule kaye kuti alowe apo bii kulibe ntchito boss Ati umakhala kuti (Biwi) Kumudzi kwanu ndikuti (Ntcheu) Oooh ndiwe ngoni Tchito yi siyukapanga suit Iwe yukupanga gwanda Kuno timalemba anthu akuzomba Nde paja wati siwe wakuzomba Olo ukasake experience vephi sitidzakulemba Experience experience experience (My foot) Experience experience experience (Uko) Experience experience experience (Yachani) Experience experience experience (Ndilibe) Experience (Igwa kumwamba) Experience (Ndingoyitola) Experience (Ibwera yokha) Experience (Ichoka Ku) Experience (Igwa kumwamba) Experience (Ndingoyitola) Experience (Ibwera yokha) Experience (Ichoka Ku)
Sanatçı: Henry Czar
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 2:52
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Henry Czar hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı