henry czar million (mandede) şarkı sözleri

Ndimafuna nditagula mansion ngati bwa kusitha Lamborghini Dollar kudzadzitsa mkatoni homie akamwe jambogin Ofcoz I will always be humble adah Chimfana cha Low-key Kupeza dollar zambiri mkumakonda beans ungathe kuphura sin Mtafika level ya Simbi Simbi Simbi angathe kusimba Simba Koma kamfana koyimba kaja Kali makola sikali lamba Ekhaya ekhaya Mpinganjila kudzandikhola Mwatchinga njira afana tidutseko tikudziwa mwayiphula Mandede! Ndede ndede ma five handede (Million million) Mandede! Ndede ndede ma five handede (Million million) Ndimafuna nditapeza handede (Million) Olo five handede (Million) Level ya mpinganjira (Billionaire) Yehovah kutsekula njira (Billion Billion) Atate! Ambuye! Mundiyakhe pephero langa Mundipatse zosowa zanga Munditsogolele Ndikamakhala ndimazadziwa kuti day inayake dzayiphula Ndikangogwadwa ndimamupepha kuti makomo atsegula Ndimayesetsa kulimbikila kuti uphawi uthepo Kuti chuma chisefukile uphawi ukhawulepo Mandede! Ndede ndede ma five handede (Million million) Mandede! Ndede ndede ma five handede (Million million) Ndimafuna nditapeza handede (Million) Olo five handede (Million) Level ya mpinganjira (Billionaire) Yehovah kutsekula njira (Billion Billion)
Sanatçı: Henry Czar
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:08
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Henry Czar hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı