icekay malawi mbuye amandikonda şarkı sözleri
Intro
Afuna nditagwa afuna nditaputwa
Afuna nditafa afuna ndingoduwa
Pre hook
Sindikhala ndimatha
Mbuye amandikonda
He is always on my side
He is always on my side
Sindikhala ndimatha
Mbuye amandikonda
He is always on my side
He is always on my side
Mbuye wanga kawawa
Palibe ofanana naye
Iye sanditaya
alindicholinga nane
Mbuye wanga kawawa
Palibe ofanana naye
Iye sanditaya
alindicholinga nane
Hook
Dani wanga amafuna ndiduke
Ndiyaluke ndiduke
Amafuna ndiduke
Ndiyaluke ndiduke
Dani wanga amafuna ndiduke
Ndiyaluke ndiduke
Amafuna ndiduke
Ndiyaluke ndiduke
Verse
Ohh Yahwe
Ndinu mbambande
U always here and u never late
Mumandipasa phavu
Ndizi confidence
Ohh Yahwe
Ndinu mbambande
U always here and u never late
Mumandipasa phavu
Ndizi confidence
U deserve all the glory
Mbuye wanga ndi one
U deserve all the glory
Mbuye wanga ndi one
Hook
Dani wanga amafuna ndiduke
Ndiyaluke ndiduke
Amafuna ndiduke
Ndiyaluke ndiduke
Dani wanga amafuna ndiduke
Ndiyaluke ndiduke
Amafuna ndiduke
Ndiyaluke ndiduke
Verse
Ambuye wanga
Mukhale nane mukhale nane
Ambuye wanga
Mukhale nane mukhale nane
I need u Lord please watch over my soul
I need u Lord please watch over my soul
Afuna nditagwa afuna nditaputwa
Afuna nditafa afuna ndingoduwa
Pre hook
Sindikhala ndimatha
Mbuye amandikonda
He is always on my side
He is always on my side
Sindikhala ndimatha
Mbuye amandikonda
He is always on my side
He is always on my side
Mbuye wanga kawawa
Palibe ofanana naye
Iye sanditaya
alindicholinga nane
Mbuye wanga kawawa
Palibe ofanana naye
Iye sanditaya
alindicholinga nane
Hook
Dani wanga amafuna ndiduke
Ndiyaluke ndiduke
Amafuna ndiduke
Ndiyaluke ndiduke
Dani wanga amafuna ndiduke
Ndiyaluke ndiduke
Outro
Amafuna ndiduke
Ndiyaluke ndiduke
Afuna nditagwa afuna nditaputwa
Afuna nditafa afuna ndingoduwa