j-mo mw bambo a ju (feat. bebesa & chaos) şarkı sözleri

Inuyo Inuyoo Leka liti inuyo Inuyooo Koma adzibambo ena Inuyo Inuyoo Leka liti inuyo Inuyooo Bambo aju bambo aju inuyoo Bambo aju bambo aju inuyoo Kaya nkhaza mzaleka liti inuyo Kaya kundidzunzaku kaya inuyo Bambo aju bambo aju inuyoo Bambo aju bambo aju inuyoo Kaya nkhaza mzaleka liti inuyo Kaya kundidzunzaku kaya inuyo Oyii yeah Inu tsiku silidutsa osandipekera nkhani Inu bambo a ju kodi vuto lanu chani Ndikati ndifunse kundimenya ngat jack chan Munthu wanji osamvera ongokhalira makani Bambo a ju inu ndati bambo a mose Lero sitigona tulo tithano tili tonse Mumangochoka pono osasiya kalikonse Mukakakhuta mowa kumafuna mudye zonse Bambo a ju izi zafika pondikwana Zomakapempha kwanu akungonditukwana Inu zomwe mumapanga mumangozunzitsana ana Munthu wamayi kudandaula musiya liti chibwana inu Bambo aju bambo aju inuyoo Bambo aju bambo aju inuyoo Kaya nkhadza mzaleka liti inuyo Kaya kundidzunzaku kaya inuyo Bambo aju bambo aju inuyoo Bambo aju bambo aju inuyoo Kaya nkhadza mzaleka liti inuyo Kaya kundidzunzaku kaya inuyo Yeah yeah Moti Mdzimukonda mkazi wanu mdzimunyadissa Nzodabwitsa mmamuuser kumbali mmakadissaa Ndeno Mkazi amangogiva akangoona pali gwero Inu munayamba kumphleya kani mumadzimva u aguero Muzifunse zomwe,mukupanganzo ndizabhobho Mukachoka mumasiya chani pakhomo? Ntchito yolera Juu ndiyanonse a bambo nda Mayi Mukhutisidwe nnzanuzo osangochulutsa, dama Ngat sakukwanitsa muphunzitseni momukonda Ndikulakwa kunyoza mkazi yemwe amakukonda Zabwino amapanga simungamupatse or zikomo Tsiku adzagwa ndeno mudzangoona ziii komo Chilichonse ndingapange chimakhala choipa kwa inu Mkazi wabwino atani tsiku ndi tsiku kundipezera zifukwa Nkhanza zanu ndalema nazo ine thupi langa langodzadza ndimabala Kwa inuyo mwina ndine mtengo kut mwina mwake sindimva kuwawa Bambo aju bambo aju inuyoo Bambo aju bambo aju inuyoo Kaya nkhadza mzaleka liti inuyo Kaya kundidzunzaku kaya inuyo Bambo aju bambo aju inuyoo Bambo aju bambo aju inuyoo Kaya nkhadza mzaleka liti inuyo Kaya kundidzunzaku kaya inuyo Inuyo Inuyoo Leka liti inuyo Inuyooo Inuyo Inuyoo Leka liti inuyo Inuyooo
Sanatçı: J-mo Mw
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 2:59
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
J-mo Mw hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı