j-mo mw uko (kagwere) (feat. waxy kay) şarkı sözleri
Yeah J-mo
Ahh ineyo asee heaa
Wa waxy hahh
Ndilibe nsampha koma wireless ndati nditchere
Ndinkhani yachuma chawo basi mmene kungachere
Alibe thandizo koma amangofuna atidyere
Tikadzudzula basi ati tikalowa jele
Asamatinamize akakhuta nsima wa
Utsogoleri ndilero utsogoleri si mawa
Zondipaka utsogoleri wamawa u k o
Osaiwala inu ana anu aja ali ku UK all
Abale anzanga abale anzanga
Mwapangitsa ndinu kut nsikana abale nsangaa
Zoti ulova wamkwana anasimbapo
Mwai wantchito anamanidwa nde amangogonana ndi azibambo
Ukoooo
Ati afuna aone nawo kagwere
Ati afuna agwire nawo ukoo
Ati afuna atchille nawo kagwere
Heee man ukoo
Ati afuna aone nawo kagwere
Ati afuna agwire nawo ukoo
Ati afuna atchille nawo
Ine uko uko uko uko ukoo
Ngati sumandidziwa ineyo ndi J-mo
Yeah mfana ovaya osadanda
Fanz yonyoza osauka kumazimva ubwana ngat shisha sandibanda
Ehh osauka alibe ntchito et? Ukoo
Inu nde ndi ofunikira (kwagwere)
Ku shoprite zodula mumangogula koma kwaosauka nde kumakanenerela?? Ukoo
Ghetto yuthi kumthira fumbi panseu
Nanga si nseu ndiwakwanu onseu
Nzanu wavutika simungamuthandize simungamumvetsetse chifukwa choti sadya kwanu??
Ukoooo
Ati afuna aone nawo kagwere
Ati afuna agwire nawo ukoo
Ati afuna atchille nawo kagwere
Heee man ukoo
Ati afuna aone nawo kagwere
Ati afuna agwire nawo ukoo
Ati afuna atchille nawo
Ine uko uko uko uko ukoo
Kuthoka ngamo tikusowa ngamo ine apa
Antchito kuwadyetsa peanut inu kudya ma mita pali chilungamo ine apa?
Ma friends okonda mabodza ukoo
Zogwira phone yanga njee ndati uko
Mazoba opanga matama uko
Zopanga nice pic pa free data uko
Zomazimva udon dada uko
Tinkacheza nawo anali anzathu asablowee adha
Tsiku silinkatha tisanatchille anali brother
Pano ati matama anaiphula ati ndi shasha
Zomatifuna time yama awards ukoo
Zomazimva dola mulibe cash nzosamveka
Nzanu wapeza mwai doors are open inu kutseka
Zomakhomererana tokhatokha ndizopusa
Umudziwe Yesu or else ukagwere uko
Ukoooo
Ati afuna aone nawo kagwere
Ati afuna agwire nawo ukoo
Ati afuna atchille nawo kagwere
Heee man ukoo
Ati afuna aone nawo kagwere
Ati afuna agwire nawo ukoo
Ati afuna atchille nawo
Ine uko uko uko uko ukoo
Ukoooo
Ati afuna aone nawo kagwere
Ati afuna agwire nawo ukoo
Ati afuna atchille nawo kagwere
Heee man ukoo
Ati afuna aone nawo kagwere
Ati afuna agwire nawo ukoo
Ati afuna atchille nawo
Ine uko uko uko uko ukoo

