madah khauya chikwama şarkı sözleri
Nkadzachitola chikwama
Yeah
Nkadzachitola chikwama
Heh
Nkadzachitola chikwama oh ooh
Nyumba iyi tidzakhoma malata
Kuseliku tidzaikila mpanda
Pakonapo tidzakumba chitsime
Nkadzachitola chikwama
Phala la mammawa tidzatsira suga
Akusukulu mudzidzavala nsapato
Moyo wanu udzakhala okoma
Oh oh nkadzachitola chikwama
Chikwama chikwama chikwama chikwama
Nanga bwanji mukuthawa ndi chikwama
Chikwama chikwama chikwama chikwama
Nanga bwanji mukuthawa ndi chikwama
Ndikadzakhala bwana
Nkadzangokhala bosi iih iih
Heh
Ndikadzakhala bwana oh ohhh
Malipiro anu tidzakweza
Palibe kuzunzika pa ntchito
Zonse zidzayenda mwa tayale
Nkadzachitola chikwama
Deile kupereka ya mmemo
Kuwerukanso nthawi yabwino
Aliyense adzakhala okondwa
Oh oh nkadzachitola chikwama oh ohh
Ooh oh yeah yeah oh
Chikwama chikwama chikwama chikwama
Nanga bwanji mukuthawa ndi chikwama
Chikwama chikwama chikwama chikwama
Nanga bwanji mukuthawa ndi chikwama
Chikwama chikwama chikwama chikwama
Nanga bwanji mukuthawa ndi chikwama
Chikwama chikwama chikwama chikwama
Nanga bwanji mukuthawa ndi chikwama
Nkadzakhala pulezidenti
Nkadzawina u M P iih iih
Ndikadzakhala khansala
Misewuyi tidzaika phula
Maulalo onse tidzakonza
Zipatala masukulu misika
Nkadzachitola chikwama
Ndithu simudzasowa chakudya
Njira zamakono zaulimi
Aliyense adzakhala okondwa
Oh oh nkadzachitola chikwama
Oh oooh oooh
Uuh
Ine nkadzachitola chikwama ooh ooh
Nanga bwanji mukuthawa ooh
Heh
Uuh
Heh
Ine nkadzachitola
Nkadzachitola
Ohhh oooh
Uh

