madah khauya chitelire şarkı sözleri
Akuchimuna nkesa munkanena motumbwa
Akuchikazi mesa munkanena monyang'wa
Kuti tsiku la ukwati ndithu mudzatimva madzi
Heh
Lero mwangoti chete tavinani tione
A ya ya ya ya ya
Akuchimuna nkesa munkanena motumbwa inuyo
Akuchikazi mesa munkanena monyada inuyo
Kuti tsiku la ukwati ndithu mudzatimva m'bebe
Heh
Lero mwangoti chete tavinani tione
A ya ya ya ya ya ya
Chite chite chite chite chitelire
Chite chite chite chite chitelire
Chite chite chite chite chitelire
Eya
Chalira tsiku laukwati
Chite chite chite chite chitelire
Chite chite chite chite chitelire
Chite chite chite chite chitelire
Eya
Chalira tsiku laukwati
A ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya
Akuchimuna mesa munkanena mwathamo
Kuti paukwati ng'ombe mbuzi mudzapha nokha
Nanga bwanji mukukanika ndikupha ndi nkhuku zomwe
Heh
Takhumudwa nanu mwatichititsa manyazi
A ya ya ya ya
Akuchimuna mesa munkanena mwathamo inuyo
Kuti paukwati ng'ombe mbuzi mudzapha nokha inuyo
Nanga bwanji mukukanika ndikuzinga n'nkhuku zomwe
Heh
Takhumudwa nanu mwatichititsa manyazi
A ya ya ya ya
Chite chite chite chite chitelire
Chite chite chite chite chitelire
Chite chite chite chite chitelire
Eya
Chalira tsiku laukwati
Chite chite chite chite chitelire
Chite chite chite chite chitelire
Chite chite chite chite chitelire
Eya
Chalira tsiku laukwati
A ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya
Akuchikazi mesa munkanena modzimva
Kuti mudzaphika thobwa lokwanila tonsefe
Nanga bwanji ena akutitu lawapelewera
Takhumudwa nanu mwatichititsa manyazi
A ya ya ya ya
Akuchikazi mesa munkanena mwathamo inuyo
Kuti mudzaphika thobwa lokwanila tonsefe inuyo
Nanga bwanji ena akutitu lawapelewera
Takhumudwa nanu mwatichititsa manyazi
A ya ya ya ya ya ya ya ya
Chite chite chite chite chitelire
Chite chite chite chite chitelire
Chite chite chite chite chitelire
Eya
Chalira tsiku laukwati
Chite chite chite chite chitelire
Chite chite chite chite chitelire
Chite chite chite chite chitelire
Eya
Chalira tsiku laukwati
A ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya
Tiye
Tiye
Tiye
A ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya ya
Tiye
Tiye
Tiye
Chitelire
Chitelire
A ya ya ya ya
Ati chalila
A ya ya ya ya
Chitelire
Chitelire
Chitelire
Chalila
Ati chalila
Chitelire
A ya ya ya ya
Chitelire
A ya ya ya ya ya
Ati chalila

