madah khauya ndiwe bwenzi şarkı sözleri
Mzanga lero kodi uli bwanji
Ndikudziwa wagwidwa ndi nthumazi
Kuti lero ndili ndi nkhani zanji
Ayi usade nkhawa
Lero ndangofuna kuti udziwe
Chikondi chako nchakuya ngati dziwe
Pokondwa polira nzanga ndiiwe
Ayi sumandithawa
Ndiwe bwenzi
Lenileni
Ndimakondwera nawe
Kupeza iwe
Monga nzanga
Ayi zedi ndi mdalitso
Lingandigwere vuto
Uli pompo
Nkakondwa ukondwa nane
Sindifunanso
Nzanga wina
Oposa m'mene ulili
Pena timatha kusamvetsetsana
Kanthawi kochepa tagwirizana
Pali zifukwa mazanamazana
Chikondi chopanda malire
Pena timatha kusamvetsetsana
Kanthawi kochepa tagwirizana
Pali zifukwa mazanamazana
Chikondi chopanda malire
Ndiwe bwenzi
Lenileni
Ndimakondwera nawe
Kupeza iwe
Monga nzanga
Ayi zedi ndi mdalitso
Lingandigwere vuto
Uli pompo
Nkakondwa ukondwa nane
Sindifunanso
Nzanga wina
Oposa m'mene ulili
Ndiwe bwenzi
Lenileni
Ndimakondwera nawe
Kupeza iwe
Monga nzanga
Ayi zedi ndi mdalitso
Lingagweee oooh
Uhh
Ohhhhhh
Uhh
Kupeza iwe ehh eh
Uhh
Lingagwe vutoo
Pompooo
Hah
Sindifunansoo ooh
Ohhh

