madah khauya uli ndi mtima şarkı sözleri
Nkazi wanga leroli ndikufunse
Wandizunguza mutu
Ndimakuzunza mjira zambirimbiri
Bwanji sumanyanyala
Ndimakhalila kukukalipira
Ngakhale pankhani zopanda pake
Umangokhalila kupepesa
Ngakhale olakwa ndili ine
Nanga nchifukwa chani
Umakhalabe ndi ine
Uli ndi mtima wachikondi sindingachipeze kwina
Ndiwe opilira pazinthu zomwe ukanatha kulira
Ngakhale pamavuto uli ndi mtima opilira
Uli ndi mtima wachikondi sindingachipeze kwina
Ndidzakhala mamuna opanda mwayi
Ndikapanda kusintha
Anthu adzanditcha olodzedwa
Ndikapanda kukonda iwe
Uli ndi china chilichonse
Chokuyenereza kukhala
Nkazi otchedwa wangwiro
Ndaona akazi aanzanga
Mamuna kulakwitsa pang'ono
Nthawi yomweyo alongedza
Ukanakhala mpikisano
Wa akazi achikondi
Bwezi uli pa number one
Iwe
Uyenera nyota yachikondi
Ah
Uuuuuhh
Ndiwe katswiri babe
Eh
Yah yah yah yah yah
Uhh
Yeh yea
Uli ndi mtima babeeeee
Uh
Ehh
Ngakhale pamavuto oh oh oh
Ah yah yah yah yah
Uli ndi mtima babeee eehiii yea yea iii
Hehhh
Uh
Ehh
Uli ndi mtima mbambande eeh eeii
Um hah
Uli ndi mtima babee
Ngakhale pamavutoo uuuh

