madalitso banda vocalist blessings follom me (feat. joe kellz) şarkı sözleri

Blessings will follow me Blessings will follow me Will follow me oya- oya -ah Never been easy nah-nah! Moyo umawawa uwu yeah I tell you ndakhalamo, mabvuto ndadutsamo Koma chaka chino ndikulengeza Madalitso mbwembwembwe Zisomo mbwembwembwe Chaka chino ndi changa Koma ngati zaka za m'mbuyo ndinkangolira Koma this year Blessings will follow me Koma ngati zaka za m'mbuyo ndinkangolira Koma this year Blessings will follow me Blessings will follow me (iiiiiii) Blessings will follow me (iiiiii) Na chaka chino eh! eh!, eh! eh! eh! Sindida nkhawa ine eh! eh! eh! eh! Ndidzingokhala ine phe eh eh eh Nkhondo amenya nda Ambuye eh! eh! eh! Chaka cha zisomo, Madalitso momo Dziko la khwidzi Blessings will follow me still oooh wo wo oh oh! Koma ngati zaka za m'mbuyo ndinkangolira Koma this year Blessings will follow me Koma ngati zaka za m'mbuyo ndinkangolira Koma this year Blessings will follow me Blessings will follow me (iiiiiii) Blessings will follow me (iiiiii) Blessings will follow me (iiiiiii) Blessings will follow me (iiiiii) Iye eh eh! iye eh! eh! Follow me, follow me Follow me, follow me
Sanatçı: MADALITSO BANDA VOCALIST
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:35
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
MADALITSO BANDA VOCALIST hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı