madalitso banda vocalist chikondi cha yesu şarkı sözleri

AaaaaHHH! Eyi Eh Eyi EH! OoooH Omama!! Chindigometsa Chikondi Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu Chikondi cha Yesu ndi chokoma Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu Chikondi cha Yesu ndi chokoma Anachoka mwamba kusiya ulemelero Kudzafera ife wabwino Yesu Chikondi chotere ndani akadaonetsa Koma Yesu adakondetsetsa ife Kupereka moyo wake kumvera kuwawa Yesu Koma Yesu akonda ife eeh- aah Ngati tili m'fulu leroli alipo anamvera kuwawa ndim'nkondetsetsa poti iye akonda ifeeee! Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu Chikondi cha Yesu ndi chokoma Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu Chikondi cha Yesu ndi chokoma Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu Chikondi cha Yesu ndi chokoma Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu Chikondi cha Yesu ndi chokoma Ooh aaah! NDdichokoma, ndichokoma. Chatipezetsa moyo aah! Dziko litachimwa Yesu anasiya zonse Kumwamba Kudzatifera wabwino Yesu Kulolera kusiya zonse kudzaombola iwe nd'ne M'bale mvetsera Yesu atikonda Ah! Yesu koma a Yesuyo, mundikondera chani ine? Ndimachimwa kulowa njira zosalungama Koma a Yesu chikondi chanu pa Ine chiyimabe Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu Chikondi cha Yesu ndi chokoma Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu Chikondi cha Yesu ndi chokoma Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu Chikondi cha Yesu ndi chokoma Chikondi cha Yesu, chikondi cha Yesu Chikondi cha Yesu ndi chokoma Chikondi cha Yesu (Chikondano chake) Chikondi cha Yesu (Chikondano chake) Chikondi cha Yesu ndi chokoma
Sanatçı: MADALITSO BANDA VOCALIST
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 4:36
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
MADALITSO BANDA VOCALIST hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı