madalitso banda vocalist mwayala gome (feat. evance meleka) şarkı sözleri

AAAAH OOH OOH AH! MMH YELELE, YELELE, HAH WAYO WAYO WAYO!! Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Mwayala gome pa maso pa adani mwadzadza chikho changa chisefuka Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Wasintha mbiri yanga mwandimveka yatsopano (yesuyo) Wandiyiwalitsa manyazi aubwana wanga (Yesuyo) Osunga pangano okwanitsa lonjezo Baba (Yesuyo) Palibe chomulaka Ine ndine mboni (Yesuyo) Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Akadapanda Yesu kukhala mbali yanga Kanamezedwa wa moyo (ayiyee) Pakuti adani anga adali maso kuti Aone kugwa kwanga (ayiyee) Leroli ali zolizoli atseka pakamwa ye Agoma nanu Yesu eh eh! Mwayala gome Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Wasintha mbiri yanga mwandimveka yatsopano (yesuyo) Wafafaniza manyazi aubwana wanga (yesuyo) Osunga pangano okwanitsa lonjezo Baba (yesuyo) Ine pano ndi umboni palibe chomulaka wandichotsa patali (yesuyo) Mwayala gome! Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka Mwayala gome pa maso pa adani Mwadzadza chikho changa chisefuka
Sanatçı: MADALITSO BANDA VOCALIST
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 5:44
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
MADALITSO BANDA VOCALIST hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı