madalitso banda vocalist pulani ya yehova şarkı sözleri

Pulani ya yehova palibe angatsutsane nayo Pulani ya yehova palibe angatsutsane nayo Palibe palibe palibe nso Palibe angatsutsane nayo Ndamva zoti mudakambilana mundigulitse Kufuna funa pulani yoti ndithe Moyo wanga ukamayenda sim'mamva bwino ah ah ndidakulakwirani chani kodi? Nde paja amati mtengo obala zipatso umagendedwa theladi ndi izi kukhala nanu bwino bwino kuyendera limodzi Koma mukusunga lupanga ku mphasa Koma choti mudziwe chomwe Yehova Adaika mwa Ine, palibe angachichotse Pulani ya yehova palibe angatsutsane nayo Pulani ya yehova palibe angatsutsane nayo Palibe palibe palibe nso Palibe angatsutsane nayo Adayesa kumpondereza mwana Davite Ali aka nkhondo sikangamenye Ankaona m'sinkhu mwa Iye mwa iye osati Yehova Mpaka nkhondo mwanayi adapambana Olo dziko liyike malire ngati Yehova walemba akwanilitsa Pulani ya yehova palibe angatsutsane nayo Pulani ya yehova palibe angatsutsane nayo Palibe palibe palibe nso Palibe angatsutsane nayo Palibe palibe palibe nso Palibe angatsutsane nayo Palibe palibe nso Palibe palibe nso yeh Onga Inu Baba Palibe palibe nso Bwana wa ma bwana Palibe palibe nso
Sanatçı: MADALITSO BANDA VOCALIST
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 5:01
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
MADALITSO BANDA VOCALIST hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı