p-tunez dzanzi şarkı sözleri
Cannot deny what I'm feeling for you
Ndiwe wekha wandichita confuse
Baby no pressure, this chance, I will not misuse
Mwina nzikutalikila cause baby you
Ndikakuganizila baby, (dzanzi)
Ngati uli pompa already (dzanzi)
Ndikakuyandikila maybe
Ngati ndikutenge ku bedi
Ukanditchula dzina
Ngati wandikhudza mu ndima
Ndipo sindifunanso wina noo
Dzanzi! Dzanzi! Dzanzi!
(From my feet to my head O)
Dzanzi! Dzanzi! Dzanzi!
(Oposa iweyo)
Ndani! Ndani! Ndani!
(Umandipasa)
Dzanzi! Dzanzi! Dzanzi!
Me I fit stammer mer mer
If you nuh give me work my Rihanna na na
Osanama ma ma, kukongola kwako nkwa matama ma ma!
Dzanzi ukandiyandikila
Ukanditalikila ndimafila nselu
Ukanditalikila
Kulakalaka nditagwira nsewu
Oh baby, baby, baby, no no no
Osandipange ineyo choncho ncho
Cause if you ever ever leave
Kumene uliko ndili konko nko!
Oh baby, baby, baby, no no no
Osandipange ineyo choncho ncho
Cause if you ever ever leave
Kumene uliko ndili konko nko!
Dzanzi! Dzanzi! Dzanzi!
(From my feet to my head O)
Dzanzi! Dzanzi! Dzanzi!
(Oposa iweyo)
Ndani! Ndani! Ndani!
(Umandipasa)
Dzanzi! Dzanzi! Dzanzi