quest mw & charisma madness anthem şarkı sözleri

Mulungu dalitsani Malawi musunge mtendele Gonjetsani adani njala nthenda ndi nsanje Eh Where you from Malawi! Pakati ku mpoto ku mmwela? Where you from Malawi Mmakonda komwe nnabadwila Where you from Malawi! Pakati ku mpoto ku mmwela? Where you from Malawi Mmakonda komwe nnabadwila Ndimakonda komwe nnabadwila Zakunja sindisilila ndine mtumbuka nde ndimanyadila Black girls ndimaiifila Wanyane kweni mulinkhuni eh? Tikamwe mowa wa nkhuni ehh! I am from Malawi phala timamwa la Likuni eh Ndanyamula mbendela mwina dziko ndikusintha ndimmene zinthu zikuyendela Osapusitsika ambuye amatikondela Tinjoye tivine gule wankulu "gule wankulu gule wankulu" Azimayi kuliza nthungululu Mulungu dalitsani Malawi musunge mtendele Gonjetsani adani njala nthenda ndi nsanje Where you from Malawi! Pakati ku mpoto ku mmwela? Where you from Malawi Mmakonda komwe nnabadwila Where you from Malawi! Pakati ku mpoto ku mmwela? Where you from Malawi Mmakonda komwe nnabadwila Ye Chariz! Dziko la mkaka ndi uchi Kwabata sungamve mifuti Timapephela nkachisi Komaso mzikiti Timalima Chamba timalima tea Tiyendeleni dindani passport Panga zotheka utenge permit Mukhala mwalandilidwa ndekuti eyyy Timamwa Malawi gin Ice kuika mchitini Lake Malawi too clean Nsomba nasiya kudya za nchitini Timadya Chambo micheni Alenje anyamula mipeni Dzanja linalo chishango Kumbuyo kuli mikondo Mulungu dalitsani Malawi musunge mtendele Gonjetsani adani njala nthenda ndi nsanje Where you from Malawi! Pakati ku mpoto ku mmwela? Where you from Malawi Mmakonda komwe nnabadwila Where you from Malawi! Pakati ku mpoto ku mmwela? Where you from Malawi Mmakonda komwe nnabadwila
Sanatçı: Quest MW & Charisma Madness
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:13
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Quest MW & Charisma Madness hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı