quest mw & charisma madness chamba or mowa şarkı sözleri

Yeah Ndikasuta chamba chamba Nzelu zanga zimakhwima Komaso ndikangomwa mowa Pena ngati nzingothima Tandiuzeni, Chabwino Nchani Chamba or mowa Chabwino nchani Chamba or mowa Ndukanika kusankha Chamba or mowa Chabwino nchani Chamba or mowa Ndukanika kusankha Chamba or mowa Ndikamwa mowa akazi amaphweka Ndikasuta chamba ndimayakhula ndekha I got a bag full of weed I got bottle of Hennessy Ndikasuta chamba sinsamba ayi sinsamba Koma Ku mowa masamba eya mmasamba Mwina chamba chindilowetsa mutchile Ndikamwa mowa madzuka ndi mmatsile Ndikasuta chamba chamba Nzelu zanga zimakwima Komaso ndikangomwa mowa Pena ngati nzingothima Tandiuzeni, Chabwino Nchani Chamba or mowa Chabwino nchani Chamba or mowa Ndukanika kusankha Chamba or mowa Chabwino nchani Ndukanika kusankha Tibanditse aise! Ndimadekha ine ndikangobanda Nde ndikangosipa zuthela jowa mpanda Komaso nduma saver kwa bush d Ndalowa mu club ndi salary tuluka ndi 2 pin Kamowa kakangogwela ku nkhwiko Nditha kukulemba ntchito Ndimasanduka chi drip donor Zizungu thoka mwa simple Ndikabanda kujowa pa stage ku show Thamangisa file dzuwa kulowa Ndimadzuka pota twenty past four Kumwa shot ndikafuna kugona Aaaah aaaaah aaaa Ine Trap life ndimaitengela Life ya n'dala ndinaitengela Ndikangoyaka ndimapepeluka koma Ndikasuta chamba chamba Nzelu zanga zimakwima Komaso ndikangomwa mowa Pena ngati nzingothima Tandiuzeni, Chabwino Nchani Chamba or mowa Chabwino nchani Chamba or mowa Ndukanika kusankha Chamba or mowa Chabwino nchani Ndukanika kusankha Chamba or mowa!!
Sanatçı: Quest MW & Charisma Madness
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:28
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Quest MW & Charisma Madness hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı