quest mw & charisma madness izi şarkı sözleri

"It looks like you lost another one" Yea aah!! Mwayi susochela Madalitso angobwela Ndimalimbikila nde ndimaikapo mtima Ali busy kunyoza ine ndungo winner Wekha tangoona izi Sizinangobwela izi Wekha tangoona izi Sizinangobwela izi I'm blessed that's why I don't stress Mwina mumadabwa ndikafika mmakometsa Uonetsetse ndimayinyetsa Sindipanga Zinthu ngati Ineyo ndikuyesa Mwayi susochela pano Ndine big fella Akufilabe bwanji zija ankati zogwela Pano akuti ndine fitititi Chifukwa ndumenya ma hitititi Got so much to say Ndungokwelabe They chanting my name like Ali bomaye Bitch get off my way Stay in your lane Sine size yako level yanga ili mmalele Mwayi susochela Madalitso angobwela Ndimalimbikila nde ndimaikapo mtima Ali busy kunyoza ine ndungo winner Wekha tangoona izi Sizinangobwela izi Wekha tangoona izi Sizinangobwela izi Ndinayamba ndikuziwa komwe ndikathele Talk is cheap sizose zomwe ine ndingavele Chomwe mafana amaziwa ndikubwata Anzanu u gangster tinatenga kwa madala You say Trappin? But you Not Trappin enough! I remember back in 19 i been up n about Gave you a feature/future put y'all niggas on map You niggas got amnesia nanga bwanji mumaiwala? Eeeh sizinangobwela izi, we used to pray for days like these Sizinangobwela izi, you should pray for days like these Mwayi susochela Madalitso angobwela Ndimalimbikila nde ndimaikapo mtima Ali busy kunyoza ine ndungo winner Wekha tangoona izi Sizinangobwela izi Wekha tangoona izi Sizinangobwela izi
Sanatçı: Quest MW & Charisma Madness
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 2:59
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Quest MW & Charisma Madness hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı