quest mw & charisma madness ndakulila şarkı sözleri

Ndinkakuphwekesa poti unkakhala pambali Ndinkangokuyesa mwina sungandithawe Ndinkakuchedwesa kumakutaisa nthawi Ndinkangoyesa mwina sungandithawe Koma pano ine ndakulila Ine ndakulila Ineyo nde ndakulila mmmh ndakulila Koma pano ine ndakulila Ine ndakulila Ubwelele ine ndakulila Aa aaaa aa aaa aaa Love of my life One of the kind Nnali Steve wonder ndinali blind Olo ndekha simpanga understand Nali ndi Mvuto, nali ndi carnal mind Chibwezi chongokhalila ma fights Zachikondi panalibepo ayi Pano ndataya chi dynamite I'm just tryna make things right yeah Kodi ngakuwine bwanji Won't play games like jumanji Babe tandipatse mtaji I like the way you call me daddy Linda bwelela, tizasungane Ndizizakuvela, kuti tisakangane You know the road when you missing home You know it's cold when the sun is gone cold! You know a lover when you let her go! You know! Oooh oooooh oh! Ndinkakuphwekesa poti unkakhala pambali Ndinkangokuyesa mwina sungandithawe Ndinkakuchedwesa kumakutaisa nthawi Ndinkangoyesa mwina sungandithawe Koma pano ine ndakulila Ine ndakulila Ineyo nde ndakulila mmmh ndakulila Koma pano ine ndakulila Ine ndakulila Ubwelele ine ndakulila Aa aaaa aa aaa aaa Zibwana nnapanga nnapanga zosiyana Pano kukuitana mamie mumandikana I need you back babe I am missing you daily Ndasowa zathu zose tinkapanga tinangosiyana malele I'm on my knees, I'm begging you I'm saying please, pano ine sindingakunamize singakuike pa easy Ayi ayi pano babe ine ndikupatsa iwe zose Ndikukonde ndi mtima wanga ndi thupi langa lose You know the road when you missing home You know it's cold when the sun is gone You know a lover when you let her go! Oooh oooooh oh! Ndinkakuphwekesa poti unkakhala pambali Ndinkangokuyesa mwina sungandithawe Ndinkakuchedwesa kumakutaisa nthawi Ndinkangoyesa mwina sungandithawe Koma pano ine ndakulila Ine ndakulila Ineyo nde ndakulila mmmh ndakulila Koma pano ine ndakulila Ine ndakulila Ubwelele ine ndakulila Aa aaaa aa aaa aaa
Sanatçı: Quest MW & Charisma Madness
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:43
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Quest MW & Charisma Madness hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı