quest mw enemizi şarkı sözleri
Zoti tinkacheza. Haaa!
Pano ndima Enemizi Enemizi Enemizi
Limodzi tinkaseka aaa K
Pano ndima Enemizi adani ma Enemizi
Anangosiya yankha phone!
Ndikayesa kuimba
Anzanga omwe amuona
Ati iye nkhani zambili akukamba
Oh yeah Oh yeah!
Switch up switch up anangosintha color character ndi crew chameleon!
Zaka zonsezi, ndinkati nzanga ndiwe
Uyuyu ndi nzanga
Uyuyu ndi nzanga
Koma njoka mu udzu khoswe mu ceiling
Zija zovuta kuziona mu m'dima
Anali anzanga
Ponda apa mpondepo
Koma pano ndima Enemizi Enemizi Enemizi
Timacheza, kulikoseko
Koma pano ndima Enemizi Enemizi Enemizi
Malingalilo a nzako ndi tsidya lina
Dzulo si lero mawaso ndi tsiku lina
Sudziwa kuti mawa libalanji
Sudziwa kuti nzako alingalila bwanji
Love your friends but don't trust em all ena amangoseka pamaso
Don't belittle nobody sudziwa adzakugwile nkono pamawa ndani
Sudziwa sudziwa aaa aaaa aaaayi sudziwa aaayi
Anangosiya yankha phone!
Ndikayesa kuimba
Anzanga omwe amuona
Ati iye nkhani zambili akukamba
Aaaayiiiii
Anali anzanga
Ponda apa mpondepo
Koma pano ndima Enemizi Enemizi Enemizi
Timacheza, kulikoseko
Koma pano ndima Enemizi Enemizi Enemizi
Zima betrayal ngati Judas ndi Jesus
Kundikana ngati Simon Petrol