quest mw ndimaganiza bho [remix] şarkı sözleri

Ndimaganiza Bho Remix Lyrics You thought I was done right? But we just getting started! Ife ndima yoh (Pre-Chorus - Spyral Mwenya) I got connects in every city and its clear Get what i want and i want it, I don't care Amangokakamila moto ndwa ifeyo (wa ifeyo!) Mfana ochedwa pa zinthu sangakhale ineyo (Chorus - Spyral Mwenya) Ndimaganiza Bho Mani Mani Ndimaganiza Bho Ndimaganiza Bho Ndimaganiza Bho Mani Mani Ndimaganiza Bho Ndimaganiza Bho Ndimaganiza Bho (Shaaaa!) Ndimaganiza Bho Ndimaganiza Bho Ndimaganiza Bho Mani Mani Ndimaganiza Bho Ndimaganiza Bho (Verse 1 - Quest) Nena ndi litilo, lomwe sinnaganize bho lo Mboni ndi pillow, sindimaganizako slow yeah Tryna make my money tall, I let my money talk Uli m'maplani talka, ulibe plani choka (go go go go) Oh my man i am just serious, ganiza mlingo opitilila Nzeru zanga m'mazithilila, ganiza bho zikuphukila Nnayiponya kutali ndipo sinnafike I'm from Malawi singabalalike Ganiza fine fine fine I need the money, panga align ma deal ku signer signer signer Show ndine headliner liner I got connects got designers Big leagues i'm not with minors Call us the ghetto runners Wakwiya azilume nsana (Verse 2 - Bee Jay) Yea Ya Ya (Mani Maniiiii) Ye! usandipase GREEN kapena SPECIAL kapena SQUASH Uzimixe kaye, paja ine ndiwama PUNCH Ndipo akuzithemba ndiwowoo? Nkona ndikuwadya LUNCH Pena ndimazidabwa kuti ndimaganiza BWANJI Koma ndimaganiza ngati Gaba daily, ndimaganiza BHO (ball) Iwe! sungaCashe kaMILLION umaganiza SLOW Ndili ndi zima bomba mphwanga ndipo ndima NYUMWISA Sinne mfana wa jonz koma ndiMAPHOURISA Mpaka fanz ifileee, fike mawa matsileee Ushashawu ndi wanga fanz ikuti Undipatsileee Muzibaye vaccine verse yanga imaMiNITSA Ndipo ine ndilibe target olo akazi ndimayimiSSa (Chorus) (Verse 3 - Spyral Mwenya) Yeah yeh! Yeah yeh! Ndimayiona bho (ball) uli mpila bwezi ine ndili Gaba Funondigwetsa pansi koma akuchepela kaba Now you wondering why the hommies calling me fada I got relatives down from Jozi to Lusaka (la familia) Lion stare on my face to show you i can be fierce Got a golden mind is why i standout from my peers Talking smack on your back, giving you these fake cheers Hommies only act nice till you get what's better than theirs (prrapapapa) Mfana wapa Malawi ndimalingalila kutali Singakhale pa mbali ndimaganiza mwa machawi Pomwe pali mbuzi pali nsuzi Ndigwile mpeni 'ne ndiphe maluzi (Verse 4 - Barry Uno) Ndimaganiza bho, Jah Jah patsogolo bho Pa ground sipali bho Suzandipeza nkuyankhila zopusa pa social media no! Suzamupeza Legendary BarryUno chasing clout for social media points Suzamupeza akucheza ndi makape, mazoba osatha flow Kutakata bho, huh Kujagula bho, huh Kugwilira no! Mwa - muna omenya mkazi timulinganize timufake ma stones Kupanga ignore huh Kupanga ignore huh Aneneri abo - dza O - fu - na ku - tisocheresa kuti ife tikathere ku moto All in all i mind my own, k'panga zondisangalasa, that Uno mode That Mdub vibe, your very own, the legendary swag that sets the tone Kutsogoza chikondi than live alone, kutsogoza umodzi so far, you are gone In God we trust, he protects his own Blessings on blessings, keep piling on (Pre-Chorus) (Verse 5 - Gwamba) Ey yo Spyral! Yo! Ndimaganiza bhooo heve nsanathoke'yi Osati kumangotokota kuti ngini ikuchoke'yi Munkati tivote mukazawina mutsitsa mafuta Pano tikufa ndi njala inu ndikumaganiza mokhuta Ndimaganiza prayer, long life ndi chi Mansion (eyiiih) Anzanu akupanga ndalama inu 'ganizila tima caption (eyiiih) Ndimaganiza Jah Jah, ndimamufila ndi passion (eyiiih) Koma sindimangoganiza'ayi ndimayika action Popanga za Yesu ndayika passion, zausatana ndayika ma sanction Fusa Versace Richmond, Entwan yeh, za Yesu zalowa fashion Ndili ndi Yesu zanga pheee Ndili ndi Yesu zanga pheeeee!
Sanatçı: Quest Mw
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 5:13
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Quest Mw hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı