sage poet compassion (feat. tadala & sagonjah) şarkı sözleri

Ey yo Sage! Popanda Chikondi sindingakhale Ndingokhala ngati mtengo oti siungabale Ukakhala opanda mano siuswa phale Chisankho ndimakonda wankulu ena burley Ena amakonda kukonda ena kukondedwa Idzamera ndi mbewu yapa nthaka or yopondedwa? Nsambi kwa wa nsembe Nsambi kwa m'Levi Dzuwa sungazembe Atelo ndi mlengi Atelo alembi Ndikukonde ngati mwini Ngakhale ukonda ngini Zopanda mwinimwini Wadyela koma wa mabala mu usinini Komabe mitima kutipula chikondi ndikufesa Zoyipa kubzikula mwazi sindikukhesa Kufunsa mafunso ngati sindikumvesa Mesa zikakuchulula zimavuta kumeza The Omnipresent Love is above so below Because Light is the electromagnetic in its form Love is alive from the moment we are born From the womb to the tomb these are lessons we should know It keeps us warm, sometimes the Love is cold Light creates and breaks the patience in the soul It's in the heart, Light is what designs in mind Love does not discriminate, Light has always been the kind God Universal, Ruler Universal Law So, no matter who you is, Light has balance of its own It's unconditional receive with no judgement It's compassion over others it's the universal coven Light workers coz Love nurtures us to the Oneness So, the path of devotion to open to door to abundance It's not far Love is not a distant star Light is Anuk Ausar, God is Love that's who we are Love Mulungu ndi chikondi ,chikondi ndi Mulungu Zinazi zipembezo anakonda munthu Chikondi ndikukonda osasankhana mtundu Chikondi ndikukonda osawonana khungu Chikondi, lamulo la Mulungu limodzi Mukonda bwanji Mulungu ngati simokonda umodzi Zonama, chikondi sichikukamba zogawa Zomanza, chikondi chikukamba zomanga Chikondi, Wadala okondedwa wakonda Kusiya kuwona chikondi ndichokongola Chikondi chilibe chilendo sichimaphonya Ngati unakhumudwa ndi chikondi chinali cha boza Chikondi ndi cha ulele, ndi cha ulele Sizongolandira nawenso upeleke Chikondi ndi anthu ndi iwe ndi ine Chikondi ndi anthu ndi ife
Sanatçı: Sage Poet
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:50
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Sage Poet hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı