sagonjah x tadala kuthokoza şarkı sözleri

Kunja kwacha, dzuwa latuluka. Anthu alowe komwe amasaka ndalama, eeh, koma tisananyamuke kumathokoza Mulungu mu zonse eeeh Kuyamika mu zonse ngakhale zonse ndi chabe Zisachite kufika poti mpakana ndikabe Zochepazi ziphukile Mtima wanga ukhutile Ngati chinga gile nkabwelela mundichingamile Zinsinsi za moyo mundiululire Zipatso za moyo mundipululire Moto wanyanya nkhuni mutifumilile Dziko kuzungulira osadabwa zizungulire Sinkumila ndikuyandama Osaodzela ndikuyang'ana Zisomo zake zingotsagana Ndinali yani dzana Lero ndine nyali dzana timangonamizana Sinditama munthu kuwopa mwina andimana Mu m'bwaa zanga ukhwepa Panga zaine mpakana mtembo useka Kumbwambwana ambwana Kumazinyenga kupambana Zako nzake zake namana kumkhwapa napana Lero ndingothokoza Mu zonse inu nditsogoza Kusekelela otonza Sazagwetsedwa otonza
Sanatçı: Sagonjah x Tadala
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:11
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Sagonjah x Tadala hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı