t-no basics şarkı sözleri

Yeah, Sibabaze yeah... Nde pali ma guys ena ake amati TNO... Kodi utulutsa single ina liti I'm like... I'm working on the basics so... Let me tell me what I'm talking about... You need to do this too... Listen... Wake up and I praise God Glad I got see another day It aint luck it's a blessing Praising God is a basic Hit the floor with knees huh Say a prayer for you leave huh God be with me please huh Kupemphera ndi ma basic Flip a page through the bible I'm a Jesus' disciple That's my ammo and my rifle Daily bread is a basic Meditate on the scriptures hearing God when he whispers Sharing whatever he teach us Evangelism is a basic Kufalitsa mawu (Yeah, yeah) Kupantha uthenga (Yeah, yeah) Wa Namalenga (Yeah, yeah) Kulalikira ndi ma basic Kukonda anzako monga iwenso osakondera (Yeah, yeah) Osalephera (Yeah, yeah), Amenewonso ndi ma basic Ndikufunika kuti, ndisayiwale maziko athu Pali zingapo Zomwe zimafunikatu Monga Mchristu Pali ziwiri zitatu Zomwe ndufunika kuti ndisayiwale ndizichitatu (Yeah yeah) Praising God is a basic Kupemphera ndi ma basic Daily bread is a basic All of these are basics Evangelism is a basic Kulalikira ndi ma basic Kukonda anzako ma basic Amenewonso ndi ma basic Praising God is a basic Kupemphera ndi ma basic Daily bread is a basic All of these are basics Evangelism is a basic Kulalikira ndi ma basic Kukonda anzako ma basic Amenewonso ndi ma basic Be a giver that's a basic It's more blessed than receiving Not because you wanna get more But you want to make a difference Wanna be a legend be a giver, everybody know that's a basic Wanna be a leader, be a servant everybody know that's a basic Kulemekeza abambo ndi amayi ako omwetu ndi ma basic Kupereka ulemu kwa munthu wamkulu kuposa iwe ndi basic Kukhala chete ndikumvetsera kaye usanayankhule ndi basic Ndiye chonde osapala Tsatanikoni ma basic Kupita ktchalitchi muzitengakotu bayibulotu ndi basic Kuyamba chibwenzi muzikhala kuti mwapemphera kaye ndi basic Osavutitsa mwana wa nzanu musanakonzeke ndi basic Osayamba zinthu popanda plan amenewa ndi ma basic Ndikufunika kuti, ndisayiwale maziko athu Pali zingapo Zomwe zimafunikatu Monga Mchristu Pali ziwiri zitatu Zomwe ndufunika kuti ndisayiwale ndizichitatu (Yeah yeah) Praising God is a basic Kupemphera ndi ma basic Daily bread is a basic All of these are basics Evangelism is a basic Kulalikira ndi ma basic Kukonda anzako ma basic Amenewonso ndi ma basic Praising God is a basic Kupemphera ndi ma basic Daily bread is a basic All of these are basics Evangelism is a basic Kulalikira ndi ma basic Kukonda anzako ma basic Amenewonso ndi ma basic Praising God is a basic Kupemphera ndi ma basic Daily bread is a basic All of these are basics Evangelism is a basic Kulalikira ndi ma basic Kukonda anzako ma basic Amenewonso ndi ma basic
Sanatçı: T-No
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:46
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
T-No hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı