t-no ntchito şarkı sözleri

Analembedwa ntchito mmmmmmm mmm mmm Analembedwa ntchito mmmmmmm mmm mmm Analembedwa ntchito mmmmmmm mmm mmm Ankasakasaka daily mmm mmm Anayipeza ntchito Ey Ey Panali nkulu wina wake Dzina lake Timoteyo Anali mnyamata wolimbika Moti anthu ambiri amatero Ankakhonza ali ku skulu Anamusankhira ku ya Ukachenjede Koma chomwe sanamuwuze N'choti ukamaliza skulu ukachenjere Ankangodziwa ngati ufuna kukhala bwana Ulimbikire skulu udakali mwana Anayesetsa ndithu nkupita college Mpaka kumaliza ntchito sanamukhole eti Ankawona ngati kuti n'chabe nthawi Idzakwana yokha sadzakhala mphawi Koma chaka mpaka chaka nkumadutsa Osapeza ntchito iye nkumafunsa Kodi ndinalakwa chani? Ndikhala lova moyo wanga wonse man? Komabe sanachite mphwayi Anaponyaponya ma CV nde mwa mwayi Analembedwa ntchito mmmmmmm mmm mmm Analembedwa ntchito mmmmmmm mmm mmm Analembedwa ntchito mmmmmmm mmm mmm Ankasakasaka daily mmm mmm Anayipeza ntchito Anasangalala atayipeza Sankhakhulupilira kuti zatheka Anayamika Mulungu nkumukweza Kukumbukira komwe akuchokera Zaka zinayi ali opanda ntchito Nkumawona ngati ndi opanda ntchito Analonjeza kuti akazayiphula Azayisamala sazayibudhula Komano nthawi nkumapita Anayamba kuyiwala ankayamika Abwana akamupatsira chokachita Amatero komatu monyinyirika Akatere Timoteyo nkumasinkha Ntchito yomweyi mpaka ine nzifinyika Ankawona ngati wafika Anasiya kulimbikira akafika M'mamawa amakhalira bhawa Masana samkhala amathawa Akampatsira Ntchito iye amakana Amvekere kuti ndiyipanga mawa Mawa lakelo litafika Anamupatsira kalata azipita Yeah Analembedwa ntchito mmmmmmm mmm mmm Analembedwa ntchito mmmmmmm mmm mmm Analembedwa ntchito mmmmmmm mmm mmm Ankasakasaka daily mmm mmm Anayipeza ntchito Ayeyiyeyiyeaaah eh Ayeyiyeyiyeaah Ayeyiyeyiyeaaah eh Ayeyiyeyiyeaah Ayeyiyeyiyeaaah eh Ayeyiyeyiyeaah Ayeyiyeyiyeaaah eh Ayeyiyeyiyeaah Anthu ambiri tikakhala mu utchimo Timakhala kuti tili pa chiphinjo Sitidziwa kuti tingasiye bwanji Timasowa mtendere muntima nanji Nde Mulungu akatipulumutsa Chisomo chke chimakhala chatikhudza Timayenera kuti timuyamike Tisayiwale popanda iye tinalibe Chikhulupiliro chathu ndi chisomo Timayenera kuti tigwire ntchito Osabwelera ku utchimo Tizidzilora kuti tife ku dziko Palibe ntchito yopanda bwana Kuti uyisunge osapanga zibwana Panga zomwe bwana wako wakutuma Osakomedwa ndi nthawi yongopuma Nde ena tili ndi ntchito Yosamala banja lathunso ndi ntchito Osangokonda ntchito yokha nkuyiwala Kuti tinkafuna banja nafe tili single Ambiri tili pa chi ntchito Osafowoka tiyeni tilimbike Ngati usakugwilira ntchito Yesu Ukugwilira ntchito winayo udziwe (Think about it) Yeah Tinalembedwa ntchito (Palibe anatikakamizatu ndi tokha) Tinalembedwa ntchito (Tinka guba tinka guba tinkagubilayeee) Tinalembedwa ntchito (Palibe anatikakamizatu ndi tokha eh) Tinkasakasaka daily (Yey yey yehh) Tinayipeza ntchito (Owoowoooh) Ayeyiyeyiyeaaah eh Ayeyiyeyiyeaah Ayeyiyeyiyeaaah eh Ayeyiyeyiyeaah Ayeyiyeyiyeaaah eh (Tinka guba tinka guba tinkagubilayeee) Ayeyiyeyiyeaah Ayeyiyeyiyeaaah eh (Woowooowooh) Ayeyiyeyiyeaah
Sanatçı: T-No
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 5:20
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
T-No hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı