T-No

Shegu (feat. EchoRino & Crucked Color)

t-no shegu (feat. echorino & crucked color) şarkı sözleri

Mmmmm Highly underrated Yeah, ih, koma TNO Echorino Crucked Color Ndinapenga kale ka Ine toto, kumwa mowa Ili ndipangano lomwe ndinalowa Bola sobo, ndikakondwa Kutchilla ndi ma members tonse tili sober Ati "iwe TNO ukufuna utinamize? Mowa ungakane titati tikulawitse?" Eya ine shegu izo nkumanzere Mayesero akabwera ife timangotere It goes like one, two, three and to the four Push temptations away when they creeping through the door Five, six, seven to the eight You can sing along if you feel like you relate Mayesero angongobwera ife timati Shegu Tchimo lingatchene bwanji ifeyo Shegu Mawonekedwe amapusisa uziti Shegu We don't do that around here Shegu Wati bwa? Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Echo kanazi aka! (Shegu) Hhm kabawa nanga? (Shegu) Ma baby awa? (Shegu) Inu ndiye Kaya amwene ndinu trad Eeh, inedi ndine trad Ndichifukwa chake zachigulugulu simpangadi Ndinapanga chisankho Chotsatila m'modzi M'modzi yemweyo anamangilira khosi sindicheukira tchimo Sine otengeka sindimadyela kunthiko Kubwera kwachisomo kunachotsa zikhomo Kodi simudabwa ndikamuvunga chi elbow? Awuze amvetse Eh, ndili ndi Yesu man Kachasu ndim'dani sitimvana man Mary-jane tidana sabweraso kwathu Osamandiyesa siine wamba munthu Pano ndine Minister shegu Yesero kubwera ili (Shegu) Mukakapopa katchimo still (Shegu) Shegu aaah! Mayesero angongobweras ife timati Shegu Tchimo lingatchene bwanji ifeyo Shegu Mawonekedwe amapusisa uziti Shegu We don't do that around here Shegu Wati bwa? Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Aaah iwe, Crucked, right up! Osapezeka pa kati-kati pamoyo ndi imfa Ndi angati-ngati amvetsela ndiyimba Zimayamba mocheza aku kodola Eko Five hands ndiwe nfana otsogola Akusungila ka mpeni kumphasa Akufuna moyo wako iwe uwuona ngat mphasha Sutha kukana bwanji Paliponse ufunthepo bwanji Sheeeegu Mabodza onse uko Timowa tonse uko Sheeeegu Kubanda konse uko Minyama yonse uko Turn your lights on Ndiwe kuwala Angaku kope za Yesu osaiwala Ena adza tsala popita kumwamba Ukapanga zunguli zunguli pama kwerelo udza tsala Shegu udzimu mvetsetsa Palibe okuletsetsa Mayesero angongobweras ife timati Shegu Tchimo lingatchene bwanji ifeyo Shegu Mawonekedwe amapusisa uziti Shegu We don't do that around here Shegu Wati bwa? Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu Shegu-shegu
Sanatçı: T-No
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:36
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
T-No hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı