t-no zamdziko (feat. regenerate) şarkı sözleri

Mmmmh yeah Mmm, yeah, yeah, listen Zamdziko lathu lapansi Sungathe kuzimvetsa Tsiku lina umapata Tsiku lina umabetsa Tsiku lina ndiwe dolo Tsiku lina ndiwe kape Nthawi zina umayima njii Nthawi zina kuopa ungagwe It's not everyday that you get it right You're constantly in a big war You want things that you can't get And when you get them then you need more I totally get how that feels Chasing highs and them cheap thrills Everyday is like a nightmare when you getting shocked with them deep chills Regret and guilt Get you feeling insane When your greatest desire's driven by personal gain But by the grace of God you get a knock on your brain All those things that you pursue you do but they're all in vain leggo Zotsaala (Iwe tamvera iwe) Osatengeka nazo zonsezi (Osatengeka iwe) Osada nkhawa (Osada nkhawa iwe) Kusinkha za mawa (Zonse zamdziko izi) Osasilira zinthu zodzasalira (Zonse zamdziko zamdziko) Zonsezi nza mdziiko oooo mmm (Zonse zamdziko zamdziko) Zonsezi nza mdziko Yaa'll Started with the little that I never had Wait, I was born naked Exactly how I'm gonna to leave this earth All I get will be donated Mpweya wobwereka Thanzi lobwereka Opportunity izichita kupatsidwa kuchokera kumwamba Yesu ndi ref, watibereka Kufuna chi nkazi cha figure, huh Ndimakonda kuwerenga Kumanga chi nyumba cha malata opindikapindika olo khwangwala osakwera denga Njale Ndinagula kale Ndi mphale Ndimafuna ngati cha a Mwale Ndi marre Ndi wale Ndinenepe Ndisalale Komabe Salary Sikukwana ndiphatikize PHd Mwina nkazi wa Thini uja ndizalande Ndiyende mayiko Nanga ndizingokhala Nyambadwe? Ndilowe Mangalande Luke Twelve vesi yake ndi ya Twenty Becoming a fool for things you can and you can't get A man's life is not found in his posessions You've got to find Christ who came for your salvation Zotsaala (Iwe tamvera iwe) Osatengeka nazo zonsezi (Osatengeka iwe) Osada nkhawa (Osada nkhawa iwe) Kusinkha za mawa (Zonse zamdziko izi) Osasilira zinthu zodzasalira (Zonse zamdziko zamdziko) Zonsezi nza mdziiko oooo mmm (Zonse zamdziko zamdziko) Zonsezi nza mdziko Iwe tamvera iwe Osatengeka iwe Osada nkhawa iwe Zonse nzamdziko izi
Sanatçı: T-No
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:15
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
T-No hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı