tadala lie lie lie şarkı sözleri

Rebel lions warfare It's on here Stand under the music to understand the music Si ine kazimvelele ongokamba za m`maluwa Anamva anthuwa Pa chiyambi panali mawu Anamveka pa chimkweza mawu Mwayi wakusintha zinthu nawu Mphuno salota anawombela mfiti m`manja Nde ndi ndani andigwile dzanja Poti zatsimikizika Zochita za anthu sizisiyanisika Atupa mimba bwa? atadya zositika Inu mboba Boys out here vala zigoba Anthu oyipa amauvala unjonda Akaona tsogolo lako lozola komba Pa maso akonda mu mtima azonda Amangonama Tigwetsa mana Koma zochitika zimasemphana Kwela pa nsanja zikundu nkumasekana Dzulo kulonjeza lero kukana Amangonama Tigwetsa mana Koma zochitika zimasemphana Kwela pa nsanja zikundu nkumasekana Dzulo kulonjeza lero kukana Mayi koto m`baleyu si njokaluzi Pali moto nkulinga utawona utsi Ali pompo until atapeza nsuzi Kunyika nsima itamangidwa mu luzi Nde ndikufunsa Ena akunena ndikutsutsa Odya ndiwo ndi ena ife kwathu nkususa Pali kwina kufasa pali kwina kupusa Munamupha Mufasa nkani Simba kulusa Timangomva zama audit zama report Milandu ingofumbwa kuma court Ndinamukhulupilira Majoti Kutaya nkhwali kamba ka manga aka nsoti Amangonama Tigwetsa mana Koma zochitika zimasemphana Kwela pa nsanja zikundu nkumasekana Dzulo kulonjeza lero kukana Amangonama Tigwetsa mana Koma zochitika zimasemphana Kwela pa nsanja zikundu nkumasekana Dzulo kulonjeza lero kukana Kutipaka nsuzi nkutijambula odya ena Ndithudi muzakumana nayo gahena Ankabwela pano tikawaona mpakanema Mbiri ndiya khoswe kadya nkena Tinamva manifesto Kalata ya Paulo yolembela Aefeso Tonse kukhala mtundu koma munthu ndi chileso M`mutu modzadza mfundu ati vuto ndi chipeso Yesa ulonjezenso Ndi mabodza omveka bwino tatengeka Chilungamo chenicheni tanyengeka Ochepa za wayendela ambiri tapweteka Amphawi taoneleledwa tapezeka Amangonama Tigwetsa mana Koma zochitika zimasemphana Kwela pa nsanja zikundu nkumasekana Dzulo kulonjeza lero kukana Amangonama Tigwetsa mana Koma zochitika zimasemphana Kwela pa nsanja zikundu nkumasekana Dzulo kulonjeza lero kukana
Sanatçı: Tadala
Türü: Belirtilmemiş
Ajans/Yapımcı: Belirtilmemiş
Şarkı Süresi: 3:33
Toplam: kayıtlı şarkı sözü
Tadala hakkında bilgi girilmemiş.

Fotoğrafı